Lord Jesus Christ and the angels to the Seven Church Ages

ZINCHITO ZA BRANHAM TABERNACLE

Cholinga ceni-ceni ca chiyanjano ca tsamba lamakina a Sierra Vista ndi kuulutsa zilankhulidwe zoonjezedwa ndi zinenedwe za makalata ndi nchito zapa Branham Tabernacle mu Jeffersonville, Indiana komwe Mbale Joseph Branham ali m’busa. Timagwizama pali modzi ndi bungwe la madikoni a Branham Tabernacle. Ngati muli ndi funso kapena zokukhuzani lumikizanani ndi dikoni, Mbale Jeremy Evans pa [email protected].

Mamasulidwe apompo sangacitike mwangwiro ndipo pafunika lamulo ili. Nchito yonse ndikuzipeleka. Kulibe kulandila ndalama kapena cosinthisa ndi nchito iyi . Abale ndi alongo awa agwira mosatopa, mosazindikilika,pa inu, mkwatibwi wa Khristu. Iwo ndi akapolo okugwirira pamodzi mu mugwirizano a mau. Tikufunirani mapemphero anu pa iwo ndi ife ndi kofunikira kwambiri pa Mbale Joseph Branham ndi banja lake.

Zinchito ziri zoyikidwa mundanda pa tsiku, ngati ili yo masulilidwa muchilankhulidwe ca. Ngati palibe omasulira, kumasulila kucitidwa ndi a Voice of God Recordings.

An Independent Church of the WORD,