21-0626 Kukhazikitsidwa #2

Uthenga: 60-0518 Kukhazikitsidwa #2

PDF

BranhamTabernacle.org

Kalata wanu mphungu

Tiyeni tonse tisonkhane pamodzi ndi kumvetsera kuwuthenge 60-0518 Kubvomerezedwa #2 sondo ino ndi nthawi ya 2:00pm, ya Jeffersonville.

Mbale Joseph Branham.

Malemba owerenga mapemphero asanayambe:
Genesis 1:26
Aefeso 1
Aroma 8:19
Agalatiya 1:6-9
Aheberi 6
Yohane 1:17