Uthenga: 65-0429b Mbewu Siidzalandira Cholowa Limodzi Ndi Mankhusu
MPHUNGU ZIKUSONKHANA PAMODZI KALATA
—–
Uthenga: 65-0429b Mbewu Siidzalandira Cholowa Limodzi Ndi Mankhusu
—–
Uthenga: 60-0522E Kukhazikitsidwa #4
Kalata wanu mphungu , tiyeni tonse tisonkhane pamodzi ndi kumvetsera Kuwuthenga Kubvomerezedwa#4 60-0522E sondo ino ndi nthawi ya 2.00pm , ya Jeffersonville.
Mbale Joseph Branham
Malemba amene owerenga uthenga usanayambe:
Aefeso 1:8-22 / 2:1 / 4:30
Ahebri 7:1-3
Genesis 14:18-24
Mateyu oyera 26:26-29
Yohane oyera 17:17
Agalatiya 1:8
Yobu 38
Uthenga: 60-0522M Kukhazikitsidwa #3
Uthenga: 60-0518 Kukhazikitsidwa #2
Tiyeni tonse tisonkhane pamodzi ndi kumvetsera kuwuthenge 60-0518 Kubvomerezedwa #2 sondo ino ndi nthawi ya 2:00pm, ya Jeffersonville.
Mbale Joseph Branham.
Malemba owerenga mapemphero asanayambe:
Genesis 1:26
Aefeso 1
Aroma 8:19
Agalatiya 1:6-9
Aheberi 6
Yohane 1:17
Uthenga: 60-0515E Kukhazikitsidwa #1
Uthenga: 65-0822M Khristu Akuwululidwa Mu Mawu Ake Omwe
Uthenga: 64-0614E Chosamvetseka