23-0212 Elyo To Ci Zyi

Mulumbe: 65-0815 Elyo To Ci Zyi

PDF

BranhamTabernacle.org

Wokondedwa Mkwati Akuyembekezera,

Ndipo ine ndikudziwa kuti, ndizakachoka pa dziko lapansi lino, matepi awo ndi mabuku amenewo adzakhala ali moyo, ndipo ambiri a inu ana aang’ono mudzapeza, mu masiku akubwela, kuti izi ziri ndendende Choonadi, chifukwa ine nachiyankhula icho mu. Dzina la Ambuye.

Bwerani mudzasonkhane nafe a Eagles, Lamlungu nthawi ya 12:00 PM. Jeffersonville nthawi, pomwe ife tikumva 65-0815,

Mubbale .Joseph Branham

An Independent Church of the WORD